KULIMA MU NJIRA YA MULUNGU

Zithunzi za kuchikutiro 

Zithunzi za kuchikutiro cha bukuli zajambulidwa kuchokera ku minda ya kulima zamasamba mu Njira ya Mulungu pafupi ndi port Elizabeth ku Sourth Africa ndi minda ina yamakono. 

Kulima mu Njira ya Mulungu 

Kulima mu Njira ya Mulungu si upangiri okha komanso dongosolo loyenera la za uzimu, kuyang’anira kwabwino ndi upangiri wamakono zomwe ndi yankho mu nkhani za ulimi, kukonzekeretsa osowa kuti achoke mu uphawi ndi zomwe Mulungu waika m`manja mwawo zomwe zikuvumbulutsa kukwaniritsa bwino kwa lonjezo la Yesu la moyo wochuluka. 

Cholinga 

Chotakasika ndi kumvera, 

komanso mizu yake yagona pa chifundo 

ndipo chikuyenera kuperekedwa ndi 

chikondi. 

Kulembanso 

Kulembanso sikukuloledwa ndi © 2017 GW Dryden 

Mungathe kupeza Ntchito iyi pa keyala ya pa intaneti iyi www.farming-gods-way.org 

Kulembanso ndi kufalitsa buku iri ngati simunasinthe china chiri chonse ndi cholinga chakuti mukaphunzitsire anthu komanso osachita malonda ndizololedwa ngakhale palibe chilolezo kuchokera kwa mwini wake koma mukuyenera osasintha dzina ndipo likuyenera kutchulidwa monga liriri munsimu. 

Kulemba kapena kuchulukitsa buku iri ndi cholinga chogulitsa ndikololedwa ngati mwapatsidwa chilolezo ndi mwini wake wolemba bukuli, 

GW. Dryden: info@farming-gods-way.org 

Katchulidwe koyenera 

Mlozo wa zamasamba mu Njira ya Mulungu, 

Dryden, GW. 2017 (kulemba kachiwiri). 

Omasulira: Dickson Shuwali 2020. 

Othandiza 

Amene anathandiza kuti buku ili lilembedwe ndi akulu akulu oyendetsa bungwe la Bountiful Grains Trust. 

Mau, kumasulira komanso kuomba mkota kwina kulikonse mu bukuli ndi kwa olemba. 

Bountiful Grains Trust, South Africa 

IT 949 / 2007 

NPO 061- 902 

PBO 930025934 

Kugula 

Kuti mupeze zipangizo za kulima mu njira ya Mulungu tsatani izi; 

Email; info@farming-gods-way.org 

Retake this course?
Retaking this course from the beginning will reset all of your tracked progress.
Retake

ALL COURSES   |   MOJA APP   |   BUSINESS   |   AGRIHUB