Kulima mu Njira ya Mulungu Mlozo Wa Masamba

Chikalatachi ndi kalozera wa ulimi wa ndiwo zamasamba ozikidwa pa mfundo za m’Baibulo ndi ntchito zaulimi wokhazikika, kutsindika kufunika kwa chilengedwe cha Mulungu ndi kasamalidwe ka nthaka.

Kulima mu Njira ya Mulungu si upangiri okha komanso dongosolo loyenera la za uzimu, kuyang’anira kwabwino ndi upangiri wamakono zomwe ndi yankho mu nkhani za ulimi, kukonzekeretsa osowa kuti achoke mu uphawi ndi zomwe Mulungu waika m`manja mwawo zomwe zikuvumbulutsa kukwaniritsa bwino kwa lonjezo la Yesu la moyo wochuluka.

Izi zikugwiritsidwa ntchito ndi chilolezo Kulima mu Njira ya Mulungu Copyright © 2017 GW Dryden

info@farming-gods-way.org

Amene anathandiza kuti buku ili lilembedwe ndi akulu akulu oyendetsa bungwe la Bountiful Grains Trust.

Retake this course?
Retaking this course from the beginning will reset all of your tracked progress.
Retake