Malawi Groundnut Guide - Chichewe
Kasamalidwe Kabwino Kwambiri Kuti Mukhale ndi Zokolola Zapamwamba
Mtedza ndi mbewu yofunika kwambiri m'Malawi muno ndipo imathandizira kuti pakhale chakudya chokwanira komanso ndalama zaulimi. Kuti alime bwino mtedzawu, alimi akuyenera kuganizira njira iliyonse yomwe ili mu bukhuli. Bukuli lilinso ndi maphukusi atatu opangira omwe alimi angasankhe malinga ndi zokolola zomwe akufuna komanso mtundu womwe akufuna, zinthu zomwe zilipo kuti agule komanso kuthekera kwawo kogula ma nputs ndi matekinoloje awa.
Wolemba ndi: Justus Chintu, Department of Agricultural Research Services - Chitedze Agricultural Research Station
Wills Munthali, ICRISAT, Lilongwe, Malawi
Rick Brandenburg, Greg Buol and David Jordan, North Carolina State University, Raleigh NC USA
Dave Hoisington and Jamie Rhoads, Peanut Innovation Lab, University of Georgia, Athens GA USA