•Keyala ya pa intaneti ya Kulima mu Njira ya Mulungu: www.farming-gods-way.org 

• Makanema a Kulima mu Njira ya Mulungu: Makanema awa amakutengerani ku mfungulo zam’Baibulo za Kulima mu Njira ya Mulungu, komanso mbali yazochitika ya upangiri ndi kuyang’anira. Makanema awa, amene anajambulidwa bwino kwambiri mu madera ena aliwonse adzamupangitsa munthu woonera kuzindikira kudabwitsa kwa chirengedwe komanso kuvundukula mphatso ya Kulima mu Njira ya Mulungu. 

• Buku la Mphunzitsi: Iri ndi buku lofunika kwambiri kwa iwo amene akufuna kuonjezera chidziwitso chawo cha Kulima mu Njira ya Mulungu. Buku iri likuyenera kukhala m’manja mwa munthu wina aliyense amene amakhumba kuphunzitsa Kulima mu Njira ya Mulungu. 

• Mulozo wa kumunda wa Kulima mu Njira ya Mulungu: Buku iri ndi mulozo wa kumunda, limene likuyenera kugwiritsidwa ntchito makamaka nthawi imene mukuphunzitsa kumudzi. Mungathe kulitenga pa intaneti yathu ya Kulima mu Njira ya Mulungu. 

• Mafunso ena mungathe kufunsa pa: info@farming-gods-way.org