1) Buku la Mphunzitsi la Kulima mu Njira ya Mulungu. GW Dryden, 2009. 

2) A-Z ya Kulima Masamba ku South Africa. J Hadfield, 2001. 

3) Ulimi osagwira ntchito, Ruth Stout, 1979. 

4) FAO- mapepala a mbewu ‘’data’’. 

5) Ulimi wa chilengedwe njira yosatembenuza nthaka. Charles Dowding, 2010. 

6) Kupanga zakudya popanda kugwiritsa ntchito mankhwala. L.J. Fuglie, 1998 

“Chiri chonse mukachichita, gwirani ntchito mochokera mumtima, monga kwa Ambuye, osati kwa anthu ayi, podziwa kuti mudzalandira kwa Ambuye mphotho ya cholowa; mutumikira Ambuye Khristu mwaukapolo.” 

Akolose 3:23,24